-
Nyimbo ya Solomo 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Undikise ndi milomo yako,
Chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo.+
-
-
Nyimbo ya Solomo 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Nditenge, tiye tithawe.
Chifukwatu mfumu yandipititsa mʼzipinda zake zamkati.
Tiye tikondwere komanso kusangalalira limodzi.
Tiye titamande* chikondi chimene umandisonyeza kuposa kutamanda vinyo.
Mpake kuti atsikana amakukonda.
-