Nyimbo ya Solomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tandiuze, iwe amene ndimakukonda kwambiri,Ndiuze kumene umakadyetsera ziweto zako,+Kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu kumutu*Pakati pa magulu a ziweto za anzako?” Nyimbo ya Solomo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
7 Tandiuze, iwe amene ndimakukonda kwambiri,Ndiuze kumene umakadyetsera ziweto zako,+Kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu kumutu*Pakati pa magulu a ziweto za anzako?”