-
1 Mafumu 14:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka nʼkumapita ndipo anafika ku Tiriza. Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira.
-
-
1 Mafumu 15:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Mʼchaka chachitatu cha Asa mfumu ya Yuda, Basa mwana wa Ahiya anakhala mfumu ya Isiraeli yense ku Tiriza ndipo analamulira kwa zaka 24.+
-