-
Nyimbo ya Solomo 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nkhuyu zoyambirira+ zapsa mumtengo wa mkuyu.
Mpesa wachita maluwa ndipo ukununkhira.
Nyamuka bwera kuno,
Wokondedwa wanga wokongola, tiye tizipita.
-