Yesaya 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Yesaya 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba. Ndinenso womaliza.+ Chivumbulutso 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
12 Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba. Ndinenso womaliza.+