-
Yesaya 44:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Munthu wosula zitsulo akugwiritsa ntchito chida chake posula chitsulo chimene wachiwotcha pamoto wamakala.
Akuchiwongola ndi hamala,
Akuchisula ndi dzanja lake lamphamvu.+
Kenako wamva njala ndipo mphamvu zake zatha.
Sanamwe madzi ndipo watopa.
-