Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Musabweretse mʼnyumba mwanu zinthu zonyansa kuti nanunso musakhale oyenera kuwonongedwa mofanana ndi zinthuzo. Muzinyansidwa nazo kwambiri komanso kuipidwa nazo chifukwa zinthu zimenezi ndi zoyenera kuwonongedwa.”

  • Deuteronomo 27:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 ‘Wotembereredwa ndi munthu aliyense wopanga chifaniziro chosema+ kapena chifaniziro chachitsulo+ nʼkuchibisa.* Chifanizirocho, chomwe ndi ntchito ya manja a mmisiri waluso,* ndi chonyansa kwa Yehova.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’*)

  • Salimo 115:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Salimo 115:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani