-
Mika 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mdani wanga adzaonanso zimenezi,
Ndipo manyazi adzagwira amene ankandinena kuti:
“Yehova Mulungu wako ali kuti?”+
Maso anga adzamuyangʼana.
Iye adzapondedwapondedwa ngati matope amumsewu.
-