Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 41:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tiuzeni zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo,

      Kuti tidziwe kuti ndinu milungu.+

      Inde, chitani chinachake, chabwino kapena choipa,

      Kuti tidabwe tikachiona.+

  • Yesaya 43:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Taonani! Ndikupanga chinthu chatsopano.+

      Ngakhale panopa chikuonekera.

      Kodi simukuchizindikira?

      Ndidzapanga njira mʼchipululu,+

      Ndipo mitsinje idzadutsa mʼchipululumo.+

  • 2 Petulo 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani