-
Yesaya 40:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chigwa chilichonse chikwezedwe mʼmwamba,
Ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe.
Malo okumbikakumbika asalazidwe,
Ndipo malo azitunda akhale chigwa.+
-