Yesaya 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo palibe amene akudziwa zimene zichitike.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu ndipo satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo. Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Anthu anga ndi opusa.+Iwo saganizira za ine. Ndi ana opusa ndipo samvetsa zinthu. Amaoneka ochenjera* akamachita zoipa,Koma sadziwa kuchita zabwino.” Ezekieli 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka. Maso ali nawo koma saona, makutu ali nawo koma samva+ chifukwa ndi anthu opanduka.+
10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo palibe amene akudziwa zimene zichitike.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu ndipo satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.
22 “Anthu anga ndi opusa.+Iwo saganizira za ine. Ndi ana opusa ndipo samvetsa zinthu. Amaoneka ochenjera* akamachita zoipa,Koma sadziwa kuchita zabwino.”
2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka. Maso ali nawo koma saona, makutu ali nawo koma samva+ chifukwa ndi anthu opanduka.+