-
Deuteronomo 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
-
-
Deuteronomo 28:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Anthu amene simukuwadziwa adzadya zipatso zamʼdziko lanu ndi mbewu zanu zonse+ ndipo nthawi zonse muzidzaberedwa mwachinyengo komanso kuponderezedwa.
-