-
Yesaya 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Chifukwa anthuwo sanabwerere kwa Mulungu amene akuwamenya,
Ndipo sanafunefune Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+
-