-
Yeremiya 50:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “Mʼmasiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,
Cholakwa cha Isiraeli chidzafufuzidwa,
Koma sichidzapezeka,” akutero Yehova.
“Machimo a Yuda sadzapezeka,
Chifukwa ine ndidzakhululukira anthu amene ndidzawasiye ndi moyo.”+
-