Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+ Yesaya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+