- 
	                        
            
            Yesaya 43:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako. Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe. 
 
-