Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+
6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+