Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 42:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 “Ineyo Yehova pofuna kusonyeza chilungamo, ndinakuitana.

      Ndakugwira dzanja.

      Ndidzakuteteza ndipo udzakhala ngati pangano pakati pa ine ndi anthu+

      Ndiponso ngati kuwala ku mitundu ya anthu,+

       7 Kuti ukatsegule maso a anthu amene ali ndi vuto losaona,+

      Kuti ukatulutse mkaidi mʼdzenje lamdima

      Ndiponso kuti anthu amene ali mumdima akawatulutse mʼndende.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani