Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 44:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo ndiponso iwe Isiraeli,

      Chifukwa ndiwe mtumiki wanga.

      Ine ndinakupanga ndipo iweyo ndiwe mtumiki wanga.+

      Iwe Isiraeli, ine sindidzakuiwala.+

  • Yeremiya 31:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Kodi Efuraimu si mwana wanga wamtengo wapatali, amene ndimamukonda?+

      Ngakhale kuti nthawi zambiri ndimamudzudzula, ndimamukonda ndipo ndimamukumbukirabe.

      Nʼchifukwa chake ndakhudzika naye* kwambiri.+

      Ndipo sindidzalephera kumumvera chisoni,” akutero Yehova.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani