Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 60:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira.

      Onse asonkhanitsidwa pamodzi. Akubwera kwa iwe.

      Ana ako aamuna akubwerabe kuchokera kutali,+

      Ndipo ana ako aakazi akubwera atanyamulidwa mʼmanja.+

  • Yesaya 66:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Adzabweretsa abale anu onse kuchokera ku mitundu yonse+ ngati mphatso kwa Yehova. Adzawabweretsa atakwera mahatchi, ngolo, ngolo zotseka pamwamba, nyulu* ndi ngamila zothamanga, mpaka kukafika kuphiri langa loyera, ku Yerusalemu. Adzachita zimenezi ngati mmene Aisiraeli amabweretsera mphatso mʼnyumba ya Yehova, ataiika mʼchiwiya choyera,” akutero Yehova.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani