Yesaya 60:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+ Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+
10 Alendo adzamanga mipanda yako,Ndipo mafumu awo adzakutumikira.+Ine ndinakulanga chifukwa ndinali nditakwiya,Koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga* ndidzakuchitira chifundo.+
16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+