-
Yesaya 60:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.
Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,
Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,
Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+
-