Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 52:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iwe Yerusalemu dzuka, sansa fumbi ndipo ukhale pampando.

      Masula zingwe zimene zili mʼkhosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni* amene unagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.+

  • Yeremiya 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwana muli ku Babulo, ndidzakusamalirani+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa pokubwezeretsani kumalo ano.’+

  • Yeremiya 50:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma Wowawombola ndi wamphamvu.+

      Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+

      Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo,+

      Kuti abweretse mtendere mʼdziko lawo+

      Ndi kusokoneza mtendere wa anthu okhala mʼBabulo.”+

  • Zekariya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma mkazi iwe, chifukwa cha magazi a pangano limene unapangana ndi ine,

      Ndidzatulutsa akaidi ako mʼdzenje lopanda madzi.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani