Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+
16 Iwe udzamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+Ndipo udzayamwa bere la mafumu.+Udzadziwadi kuti ine Yehova ndine Mpulumutsi wako,Ndiponso kuti Wamphamvu wa Yakobo ndi Wokuwombola.+