Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 44:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kuti akwaniritsidwe

      Ndiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene amithenga anga analosera.+

      Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+

      Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+

      Ndipo ndidzakonza malo ake amene anawonongedwa.’+

  • Yesaya 61:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iwo adzamanganso malo amene akhala bwinja kwa nthawi yaitali.

      Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale,+

      Adzakonzanso mizinda imene inawonongedwa,+

      Malo amene akhala ali osakazidwa kumibadwomibadwo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani