-
Yesaya 50:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.
Ndi ndani amene adzanene kuti ndine wolakwa?
Onse adzatha ngati chovala.
Njenjete* idzawadya.
-