Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ekisodo 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Nehemiya 9:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno munakhaulitsa Farao, atumiki ake onse ndiponso anthu onse amʼdziko lake powaonetsa zizindikiro ndi zodabwitsa.+ Munachita zimenezi chifukwa munadziwa kuti iwo anachita zinthu modzikuza+ kwa makolo athu. Pamenepa munadzipangira dzina lomwe lilipobe mpaka lero.+ 11 Munagawa nyanja pamaso pawo ndipo anadutsa panthaka youma.+ Anthu amene ankawathamangitsa munawaponya pansi pa nyanja ngati mwala woponyedwa mʼmafunde amphamvu.+

  • Salimo 106:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Ezekieli 29:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Umuuze kuti: ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Ine ndikulanga iwe Farao mfumu ya Iguputo,+

      Iwe chilombo chachikulu chamʼnyanja chimene chagona mʼngalande zotuluka mumtsinje wake wa Nailo,+

      Ndipo wanena kuti, ‘Mtsinje wa Nailo ndi wanga.

      Ineyo ndinaupanga ndekha.’+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani