Ezara 1:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+ Yesaya 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe Yerusalemu dzuka, sansa fumbi ndipo ukhale pampando. Masula zingwe zimene zili mʼkhosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni* amene unagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.+
20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
2 Iwe Yerusalemu dzuka, sansa fumbi ndipo ukhale pampando. Masula zingwe zimene zili mʼkhosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni* amene unagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.+