Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 60:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.

      Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,

      Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,

      Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+

  • Yeremiya 31:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Pangano limene ndidzapangane ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika chilamulo changa mwa iwo+ ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+

  • Zekariya 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani