-
Salimo 137:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Chifukwa kumeneko, anthu amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+
Amene ankatinyozawo ankafuna kuti tiwasangalatse. Iwo anati:
“Tiimbireni nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.”
-