-
Ezekieli 20:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Kenako mudzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzakuchitirani zimenezi chifukwa cha dzina langa+ osati mogwirizana ndi khalidwe lanu loipa kapena zinthu zoipa zimene munkachita, inu a nyumba ya Isiraeli,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-