-
Levitiko 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire, iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.
-