-
Amosi 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera
Pamene ndidzatumiza njala mʼdziko.
Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,
Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+
-