Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse azidzaphunzitsidwa ndi Yehova,+Ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+ Yesaya 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika