-
Yeremiya 34:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova analankhula ndi Yeremiya pambuyo poti Mfumu Zedekiya yachita pangano ndi anthu onse a mu Yerusalemu kuti alengeze ufulu,+ 9 kuti aliyense amasule akapolo ake a Chiheberi, aamuna ndi aakazi, kuti pasapezeke munthu amene akusunga Myuda mnzake ngati kapolo wake.
-