Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 32:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chifukwa munthu wopusa adzalankhula zinthu zopanda nzeru,

      Ndipo mtima wake udzaganiza zochita zinthu zopweteka ena.+

      Iye adzachita zimenezi kuti alimbikitse mpatuko* komanso kuti azinenera Yehova zinthu zoipa,

      Kuti achititse munthu wanjala kukhala wopanda chakudya

      Ndiponso munthu waludzu kukhala wopanda chilichonse choti amwe.

  • Yesaya 59:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Chifukwa mʼmanja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi+

      Ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa.

      Milomo yanu imalankhula zabodza+ ndipo lilime lanu limanena zinthu zopanda chilungamo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani