-
Yeremiya 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mofanana ndi chitsime chimene chimatulutsa madzi ozizira,
Yerusalemu amatulutsanso zinthu zoipa.
Mkati mwake mukumveka phokoso la chiwawa komanso kuponderezana.+
Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.
-