- 
	                        
            
            Yesaya 31:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
 - 
                            
- 
                                        
6 “Aisiraeli inu, bwererani kwa Mulungu amene mwamupandukira mopanda manyazi.+
 
 - 
                                        
 
- 
	                        
            
            Yesaya 32:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
 - 
                            
- 
                                        
6 Chifukwa munthu wopusa adzalankhula zinthu zopanda nzeru,
Ndipo mtima wake udzaganiza zochita zinthu zopweteka ena.+
Iye adzachita zimenezi kuti alimbikitse mpatuko* komanso kuti azinenera Yehova zinthu zoipa,
Kuti achititse munthu wanjala kukhala wopanda chakudya
Ndiponso munthu waludzu kukhala wopanda chilichonse choti amwe.
 
 - 
                                        
 
- 
	                        
            
            Yeremiya 17:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
 - 
                            
- 
                                        
13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,
Onse amene akukusiyani adzachita manyazi.
 
 -