-
Yobu 34:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa iye amapereka mphoto kwa munthu mogwirizana ndi zimene amachita,+
Ndipo amamusiya kuti akumane ndi mavuto chifukwa cha zochita zake.
-