-
Yoweli 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha.
Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+
Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri.
-