-
Deuteronomo 1:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Komanso munaona mʼchipululu mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake. Ankakunyamulani kulikonse kumene munkapita mpaka kudzafika pamalo ano.’
-