Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+