Yesaya 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa iwo adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene munkailakalaka,+Ndipo mudzachititsidwa manyazi chifukwa cha minda imene munasankha.*+ Yesaya 66:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.
29 Chifukwa iwo adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene munkailakalaka,+Ndipo mudzachititsidwa manyazi chifukwa cha minda imene munasankha.*+
17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.