-
Yesaya 60:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.
Adzatenga dzikoli kukhala lawo mpaka kalekale.
-
-
Ezekieli 37:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiye uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga Aisiraeli kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumbali zonse ndipo ndidzawabweretsa mʼdziko lawo.+
-