Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 28:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya zamʼnyumba ya Mulungu woona+ nʼkuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko za nyumba ya Yehova.+ Kenako anadzimangira maguwa ansembe mʼmakona onse a mu Yerusalemu.

  • 2 Mbiri 34:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 chifukwa chakuti andisiya+ nʼkumakapereka nsembe zautsi kwa milungu ina kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo, ndibweretsa mkwiyo wanga pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani