-
2 Mafumu 16:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako Ahazi anatenga siliva ndi golide wapanyumba ya Yehova ndiponso wochokera mʼnyumba ya mfumu nʼkutumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+ 9 Mfumu ya Asuri inamvera pempho lake ndipo inapita ku Damasiko nʼkukalanda mzindawo. Anthu amumzindawo inawagwira nʼkupita nawo ku Kiri+ ndipo Rezini inamupha.+
-
-
Yesaya 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino, mayiko a mafumu awiri amene ukuchita nawo manthawo, adzakhala atasiyidwiratu.+
-