Yesaya 54:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.
54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.