-
2 Mafumu 18:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kenako Rabisake anaimirira nʼkulankhula mokweza mʼchilankhulo cha Ayuda kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+
-
-
2 Mafumu 18:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ndi mulungu uti pa milungu yonse ya mayiko, amene wapulumutsa dziko lake mʼmanja mwanga, kuti Yehova athe kupulumutsa Yerusalemu mʼmanja mwanga?”’”+
-