Deuteronomo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa nʼkupita kudziko lina,+ ndipo adzakuchitirani chifundo+ nʼkukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+ Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, dziko lanu mwalisonyeza kukoma mtima.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ukapolo.+ Salimo 126:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.*Muuzeni kuti ntchito imene ankagwira mokakamizidwa yatha,Komanso kuti malipiro a zolakwa zake aperekedwa.+ Kuchokera mʼdzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira* a machimo ake onse.”+ Yesaya 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa nʼkupita kudziko lina,+ ndipo adzakuchitirani chifundo+ nʼkukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+
85 Inu Yehova, dziko lanu mwalisonyeza kukoma mtima.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ukapolo.+
2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.*Muuzeni kuti ntchito imene ankagwira mokakamizidwa yatha,Komanso kuti malipiro a zolakwa zake aperekedwa.+ Kuchokera mʼdzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira* a machimo ake onse.”+