Yeremiya 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Taonani! Hamala yophwanyira mitundu ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa nʼkuwonongedwa.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chochititsa mantha pakati pa anthu a mitundu ina.+
23 Taonani! Hamala yophwanyira mitundu ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa nʼkuwonongedwa.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chochititsa mantha pakati pa anthu a mitundu ina.+